Levitiko 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa moyo wa nyama uli mʼmagazi+ ndipo ine ndawapereka paguwa lansembe+ kuti azikuphimbirani machimo. Zili choncho chifukwa magazi ndi amene amaphimba machimo+ chifukwa cha moyo umene uli mʼmagaziwo. Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:11 ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’, tsa. 75 Nsanja ya Olonda,6/15/2004, ptsa. 15-166/15/1991, tsa. 9
11 Chifukwa moyo wa nyama uli mʼmagazi+ ndipo ine ndawapereka paguwa lansembe+ kuti azikuphimbirani machimo. Zili choncho chifukwa magazi ndi amene amaphimba machimo+ chifukwa cha moyo umene uli mʼmagaziwo.
17:11 ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’, tsa. 75 Nsanja ya Olonda,6/15/2004, ptsa. 15-166/15/1991, tsa. 9