Genesis 46:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ana a Yuda+ anali Ere,+ Onani,+ Shela,+ Perezi,+ ndi Zera.+ Komabe, Ere ndi Onani anafera kudziko la Kanani.+ Ana a Perezi anali Hezironi+ ndi Hamuli.+ 1 Mbiri 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamara+ mpongozi wake ndiye anam’berekera Perezi+ ndi Zera. Ana onse a Yuda anali asanu.
12 Ana a Yuda+ anali Ere,+ Onani,+ Shela,+ Perezi,+ ndi Zera.+ Komabe, Ere ndi Onani anafera kudziko la Kanani.+ Ana a Perezi anali Hezironi+ ndi Hamuli.+