1 Samueli 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno zimene zinachitika n’zakuti, pamene Sauli anali kulankhula ndi wansembe,+ chipwirikiti mumsasa wa Afilisiti chinapitiriza kuwonjezeka, ndipo chinali kukulirakulira. Kenako Sauli anauza wansembeyo kuti: “Basi, siya zimenezi.”
19 Ndiyeno zimene zinachitika n’zakuti, pamene Sauli anali kulankhula ndi wansembe,+ chipwirikiti mumsasa wa Afilisiti chinapitiriza kuwonjezeka, ndipo chinali kukulirakulira. Kenako Sauli anauza wansembeyo kuti: “Basi, siya zimenezi.”