Numeri 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Itanitsa fuko la Levi+ ndipo uwapereke kwa wansembe Aroni kuti azimutumikira.+ Numeri 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi ndi chinthu chaching’ono kuti Mulungu anakuyandikizani kwa iye, limodzi ndi abale anu onse, ana a Levi? Kodi tsopano anthu inu mukufunanso udindo waunsembe?+ 1 Mbiri 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa nthawi imeneyi m’pamene Davide ananena kuti: “Alevi okha ndiwo ayenera kunyamula likasa la Mulungu woona, chifukwa Yehova anasankha iwowa kuti azinyamula likasa la Yehova+ ndi kum’tumikira+ mpaka kalekale.”*
10 Kodi ndi chinthu chaching’ono kuti Mulungu anakuyandikizani kwa iye, limodzi ndi abale anu onse, ana a Levi? Kodi tsopano anthu inu mukufunanso udindo waunsembe?+
2 Pa nthawi imeneyi m’pamene Davide ananena kuti: “Alevi okha ndiwo ayenera kunyamula likasa la Mulungu woona, chifukwa Yehova anasankha iwowa kuti azinyamula likasa la Yehova+ ndi kum’tumikira+ mpaka kalekale.”*