2 “Lamula ana a Isiraeli kuti pacholowa chawo cha malo, akapatseko Alevi mizinda+ yokhalamo. Akaperekenso kwa Aleviwo malo onse odyetserako ziweto ozungulira mizindayo.+
54 Otsatirawa ndiwo malo amene ankakhala ana a Aroni a m’banja la Akohati,+ m’misasa yawo yokhala ndi mipanda m’madera awo,+ chifukwa maere anagwera iwowo: