1 Mafumu 22:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mukawauze kuti, ‘Mfumu yanena kuti:+ “Kam’tsekereni munthu uyu.+ Muzim’patsa chakudya chochepa+ ndi madzinso ochepa, kufikira ine nditabwerera mu mtendere.”’”+
27 Mukawauze kuti, ‘Mfumu yanena kuti:+ “Kam’tsekereni munthu uyu.+ Muzim’patsa chakudya chochepa+ ndi madzinso ochepa, kufikira ine nditabwerera mu mtendere.”’”+