Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 11:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Kenako Yehova anatsika mumtambo+ n’kulankhula naye.+ Anatengako gawo lina la mzimu+ umene unali pa Mose n’kuuika pa aliyense wa akulu 70 amenewo. Ndipo mzimuwo utangokhala pa iwo, anayamba kuchita zinthu ngati aneneri, koma sanadzachitenso kachiwiri.+

  • 2 Mbiri 15:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Tsopano mzimu+ wa Mulungu unafikira Azariya mwana wa Odedi.+

  • 2 Mbiri 24:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Tsopano mzimu wa Mulungu+ unadzaza+ Zekariya+ mwana wa wansembe Yehoyada+ ndipo anaimirira pamalo okwera, n’kuyamba kuuza anthuwo kuti: “Mulungu woona wanena kuti, ‘N’chifukwa chiyani mukuphwanya malamulo a Yehova? Kodi simukuona kuti zinthu sizikukuyenderani bwino?+ Popeza mwamusiya Yehova, iyenso akusiyani.’”+

  • 2 Petulo 1:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Chifukwa ulosi sunayambe wanenedwapo mwa kufuna kwa munthu,+ koma anthu analankhula mawu ochokera kwa Mulungu+ motsogoleredwa ndi mzimu woyera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena