2 Mbiri 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho Yahazieli anati: “Tamverani Ayuda nonsenu, anthu okhala mu Yerusalemu, ndi inu Mfumu Yehosafati! Izi n’zimene Yehova wanena kwa inu, ‘Musaope+ kapena kuchita mantha ndi khamu lalikululi, popeza nkhondoyi si yanu ndi ya Mulungu.+
15 Choncho Yahazieli anati: “Tamverani Ayuda nonsenu, anthu okhala mu Yerusalemu, ndi inu Mfumu Yehosafati! Izi n’zimene Yehova wanena kwa inu, ‘Musaope+ kapena kuchita mantha ndi khamu lalikululi, popeza nkhondoyi si yanu ndi ya Mulungu.+