Ekisodo 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mphamvu ndi nyonga yanga ndi Ya,*+ pakuti wandipulumutsa.+Ameneyu ndi Mulungu wanga, ndidzam’tamanda.+ Ndiye Mulungu wa atate anga,+ ndidzam’kweza.+ 2 Samueli 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anati:“Yehova ndiye thanthwe langa,+ malo anga achitetezo+ ndiponso Wopereka chipulumutso kwa ine.+ Salimo 103:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 103 Tamanda Yehova, iwe moyo wanga.+Chilichonse mkati mwanga, chitamande dzina lake loyera.+
2 Mphamvu ndi nyonga yanga ndi Ya,*+ pakuti wandipulumutsa.+Ameneyu ndi Mulungu wanga, ndidzam’tamanda.+ Ndiye Mulungu wa atate anga,+ ndidzam’kweza.+
2 Iye anati:“Yehova ndiye thanthwe langa,+ malo anga achitetezo+ ndiponso Wopereka chipulumutso kwa ine.+