Ekisodo 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo Mose anamanga guwa lansembe n’kulitcha kuti Yehova-nisi,* 1 Samueli 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako Samueli anatenga mwala+ ndi kuuimika pakati pa Mizipa ndi Yesana ndipo anautcha dzina lakuti Ebenezeri,* n’kunena kuti: “Lero Yehova watithandiza ngati kale.”+
12 Kenako Samueli anatenga mwala+ ndi kuuimika pakati pa Mizipa ndi Yesana ndipo anautcha dzina lakuti Ebenezeri,* n’kunena kuti: “Lero Yehova watithandiza ngati kale.”+