2 Mbiri 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova anapitiriza kukhala ndi Yehosafati+ chifukwa anayenda m’njira zimene Davide kholo lake+ anayenda kalekale, ndipo sanafunefune Abaala.+ Salimo 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti ndasunga njira za Yehova,+Sindinachoke kwa Mulungu wanga. Ndikanatero, ndikanachita chinthu choipa.+
3 Yehova anapitiriza kukhala ndi Yehosafati+ chifukwa anayenda m’njira zimene Davide kholo lake+ anayenda kalekale, ndipo sanafunefune Abaala.+
21 Pakuti ndasunga njira za Yehova,+Sindinachoke kwa Mulungu wanga. Ndikanatero, ndikanachita chinthu choipa.+