1 Mafumu 22:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Panali pa nthawi imeneyo pamene Ahaziya mwana wa Ahabu anapempha Yehosafati kuti: “Bwanji antchito anga apite pamodzi ndi antchito anu m’zombozo?” Koma Yehosafati anakana.+ 1 Akorinto 15:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Musasocheretsedwe. Kugwirizana ndi anthu oipa kumawononga makhalidwe abwino.+
49 Panali pa nthawi imeneyo pamene Ahaziya mwana wa Ahabu anapempha Yehosafati kuti: “Bwanji antchito anga apite pamodzi ndi antchito anu m’zombozo?” Koma Yehosafati anakana.+