Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Akorinto 15
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

1 Akorinto 15:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aga 1:11
  • +Mac 18:11
  • +Aro 5:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, ptsa. 14-15

1 Akorinto 15:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 1:16
  • +Aga 3:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, ptsa. 14-15

1 Akorinto 15:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aga 1:12
  • +Sl 22:15; Yes 53:8, 12; Da 9:26; 1Pe 2:24

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 3

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, ptsa. 14-15

    2/15/1991, tsa. 5

1 Akorinto 15:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yes 53:9; Mt 27:60
  • +Mt 28:7
  • +Lu 24:46
  • +Sl 16:10; Yes 53:10; Yon 2:10

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 3

1 Akorinto 15:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Lu 24:34
  • +Yoh 20:26

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 3

    Nsanja ya Olonda,

    3/1/2013, tsa. 4

    4/1/2010, tsa. 25

    7/1/1998, ptsa. 14-15

    1/15/1988, tsa. 30

    Tsanzirani, tsa. 202

    Mawu a Mulungu, ptsa. 82-86

1 Akorinto 15:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mt 28:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    “Wotsatira Wanga,” tsa. 97

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 3

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    7/2019, tsa. 14

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2015, ptsa. 26-27

    7/1/1998, ptsa. 14-16

    10/1/1995, tsa. 14

    5/1/1991, tsa. 8

    Yesu—Ndi Njira, tsa. 310

    Mawu a Mulungu, ptsa. 82-86

1 Akorinto 15:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 12:17
  • +Mac 1:2, 6

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Muzikonda Anthu, lesson 8

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    1/2022, ptsa. 9-10

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 112

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 3

    Nsanja ya Olonda,

    3/15/2014, ptsa. 4-5

    7/1/1998, ptsa. 14-16

    Mawu a Mulungu, ptsa. 82-86

1 Akorinto 15:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 9:4; 1Ak 9:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    9/2022, tsa. 27

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 3

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2000, tsa. 29

    7/1/1998, ptsa. 14-16

    Mawu a Mulungu, ptsa. 82-86

1 Akorinto 15:9

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aef 3:8
  • +Mac 8:3; Aga 1:13; 1Ti 1:13

1 Akorinto 15:10

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aef 4:7
  • +2Ak 6:1
  • +2Ak 11:23
  • +Afi 2:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/2013, ptsa. 23-24

    8/1/2000, tsa. 14

1 Akorinto 15:11

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 18:10

1 Akorinto 15:12

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 4:2; 17:31
  • +Mt 22:23; Mac 26:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 5

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, ptsa. 14, 16-17

    8/15/1997, tsa. 12

    8/1/1993, tsa. 16

    9/15/1990, tsa. 25

1 Akorinto 15:13

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 10:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    3/1/2013, tsa. 4

1 Akorinto 15:14

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1At 4:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    3/1/2013, tsa. 4

    8/15/1997, tsa. 12

1 Akorinto 15:15

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 3:15
  • +Mac 1:22
  • +Mac 2:24; 4:10; 13:30
  • +Mac 17:31; 1Ak 6:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    3/1/2013, tsa. 4

1 Akorinto 15:17

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 4:25; Ahe 7:25

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    3/1/2013, tsa. 4

    7/1/1998, ptsa. 16-17

1 Akorinto 15:18

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Mac 7:59
  • +1Ak 15:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, ptsa. 5-6

    Nsanja ya Olonda,

    3/1/2013, tsa. 4

    7/1/1998, ptsa. 16-17

1 Akorinto 15:19

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yoh 1:12

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    3/1/2013, tsa. 4

    7/1/1998, ptsa. 16-17

1 Akorinto 15:20

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Pe 1:3
  • +Le 23:10; Akl 1:18
  • +Mac 26:23

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, ptsa. 5-6

    Nsanja ya Olonda,

    3/1/2013, tsa. 7

    7/15/2007, tsa. 26

    7/15/2000, ptsa. 13-14

    7/1/1998, tsa. 17

    3/1/1998, tsa. 13

    1/1/1987, tsa. 25

1 Akorinto 15:21

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 3:19
  • +Yoh 11:25

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 5

    Nsanja ya Olonda,

    3/1/2013, tsa. 7

    7/1/1998, tsa. 17

1 Akorinto 15:22

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 5:12
  • +Aro 5:17; 6:23

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, ptsa. 5-6, 30

    Nsanja ya Olonda (Yogawira),

    No. 2 2017, tsatsa. 5-6

    Nsanja ya Olonda,

    3/1/2013, tsa. 7

    7/1/1998, tsa. 17

    Kukambitsirana, tsa. 95

1 Akorinto 15:23

Mawu a M'munsi

  • *

    Onani Zakumapeto 8.

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 1:5
  • +Mt 24:3; 25:31; 1At 4:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 6

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2017, ptsa. 11-12

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2007, tsa. 26

    7/15/2000, ptsa. 13-14

    7/1/1998, ptsa. 17, 22-24

    10/1/1986, ptsa. 25-26

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, ptsa. 172-173

1 Akorinto 15:24

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 110:2; Da 2:44

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 291, 300

    Lambirani Mulungu, tsa. 189

    Nsanja ya Olonda,

    10/15/2000, tsa. 20

    7/1/1998, tsa. 21

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 182

    Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 180-182

1 Akorinto 15:25

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 110:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    10/1/1986, tsa. 25

1 Akorinto 15:26

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 20:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 30

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, ptsa. 6-7

    Nsanja ya Olonda,

    9/15/2014, ptsa. 23-27

    9/15/2012, tsa. 11

    7/1/1998, ptsa. 21-22

    10/1/1986, tsa. 25

    Ufumu wa Mulungu Ukulamulira, tsa. 237

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 291, 300

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 182

1 Akorinto 15:27

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 8:6; Aef 1:22
  • +Ahe 2:8
  • +1Pe 3:22

1 Akorinto 15:28

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Afi 3:21
  • +Yoh 3:35; 14:28
  • +1Ak 3:23

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Utumiki Komanso Moyo Wathu,

    4/2019, tsa. 6

    Nsanja ya Olonda,

    9/15/2014, tsa. 27

    9/15/2012, ptsa. 11-12

    12/1/2007, tsa. 30

    7/1/1998, tsa. 22

    6/1/1994, ptsa. 30-31

    Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 180-189

1 Akorinto 15:29

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 6:4
  • +Mac 17:31
  • +1Ak 12:13; Aga 3:27

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 14

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2008, tsa. 27

    10/1/2003, tsa. 29

    8/15/2000, tsa. 30

    7/15/2000, tsa. 17

    7/1/1998, ptsa. 17-18

    Kukambitsirana, ptsa. 366-367

1 Akorinto 15:30

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 8:36; 2Ak 11:26

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, ptsa. 17-18

1 Akorinto 15:31

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 4:9
  • +1At 2:19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, tsa. 18

1 Akorinto 15:32

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +2Ak 1:8
  • +Yes 22:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 163

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 9

    Nsanja ya Olonda,

    3/1/2013, tsa. 3

    10/15/2007, tsa. 3

    6/15/2002, ptsa. 26-28

    7/15/2000, tsa. 18

    7/1/1998, tsa. 18

    11/1/1997, ptsa. 24-25

    8/15/1997, tsa. 12

    11/1/1996, tsa. 16

    9/15/1990, tsa. 25

    2/15/1989, tsa. 5

    6/15/1988, ptsa. 18-19

1 Akorinto 15:33

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Miy 13:20; 1Ak 5:6; 2Pe 2:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    2/2023, ptsa. 17-18

    Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 48

    Galamukani!,

    No. 3 2019, tsa. 9

    9/8/2005, ptsa. 13-14

    8/8/2005, ptsa. 11-13

    3/8/1997, tsa. 24

    1/8/1994, ptsa. 16-17

    2/8/1990, tsa. 27

    Nsanja ya Olonda,

    8/15/2015, ptsa. 25-26

    7/15/2012, tsa. 15

    5/1/2007, ptsa. 15-16

    3/15/2006, tsa. 23

    7/15/2000, tsa. 18

    7/1/1998, tsa. 18

    11/1/1997, ptsa. 23-25

    7/15/1997, tsa. 18

    2/1/1994, tsa. 17

    8/1/1993, ptsa. 15-20

    8/15/1991, tsa. 29

    7/15/1991, ptsa. 23-24

    6/15/1988, ptsa. 18-19

    3/15/1987, tsa. 6

    Tsiku la Yehova, ptsa. 134-136

1 Akorinto 15:34

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 13:11; Aef 5:14
  • +1At 4:5
  • +1Ak 6:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, tsa. 18

    6/15/1988, ptsa. 18-19

1 Akorinto 15:35

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Yo 3:2

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, ptsa. 10-11

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2000, tsa. 18

    7/1/1998, tsa. 19

1 Akorinto 15:36

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yoh 12:24

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, ptsa. 19-20

1 Akorinto 15:37

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 1:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 10

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, ptsa. 19-20

1 Akorinto 15:38

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 1:12
  • +1Ak 12:18

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 10

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, ptsa. 19-20

1 Akorinto 15:39

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 1:28

1 Akorinto 15:40

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 22:11; Da 7:10
  • +Ge 2:7; Ahe 2:7
  • +Mt 28:3; Lu 24:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, ptsa. 10-11

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2000, tsa. 18

    7/1/1998, tsa. 20

1 Akorinto 15:41

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Sl 72:5
  • +Ge 1:16
  • +Da 12:3

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, ptsa. 10-11

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, tsa. 20

    6/15/1993, tsa. 11

1 Akorinto 15:42

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yoh 12:25
  • +Aro 2:7

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 11

    Nsanja ya Olonda,

    7/15/2000, tsa. 18

    7/1/1998, tsa. 20

1 Akorinto 15:43

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yoh 17:14
  • +Akl 3:4
  • +1Ak 1:27
  • +Chv 20:4

1 Akorinto 15:44

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Ak 6:13
  • +Yoh 14:3

1 Akorinto 15:45

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 2:7
  • +1Ti 3:16
  • +Yoh 5:26

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Yandikirani, tsa. 145

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 11

    Nsanja ya Olonda,

    9/15/2014, tsa. 26

    3/15/2000, tsa. 4

    2/15/1991, tsa. 14

    7/15/1990, tsa. 23

    8/15/1989, ptsa. 11-12, 13-14

    Galamukani!,

    5/8/2005, tsa. 16

    Mphunzitsi Waluso, ptsa. 192-193

    Kukambitsirana, tsa. 26

    Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 163-164, 169

1 Akorinto 15:46

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Pe 3:18

1 Akorinto 15:47

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 3:19
  • +Yoh 3:13; 6:33

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/1991, tsa. 14

    Kukambitsirana, tsa. 26

1 Akorinto 15:48

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 2:7
  • +Afi 3:20
  • +Afi 3:21

1 Akorinto 15:49

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ge 5:3
  • +Aro 8:29

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 11

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, tsa. 20

1 Akorinto 15:50

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yoh 3:3
  • +1Pe 1:23

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 11

    Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2145

    Nsanja ya Olonda,

    1/15/1993, tsa. 6

1 Akorinto 15:51

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1At 4:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 12

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, tsa. 17

    2/15/1995, tsa. 22

    1/15/1993, tsa. 6

    Kukhala ndi Moyo Kosatha, tsa. 173

1 Akorinto 15:52

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1At 4:16

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 12

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, tsa. 17

    2/15/1995, tsa. 22

    1/15/1993, tsa. 6

1 Akorinto 15:53

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 2:7
  • +Aro 8:11; 2Ak 5:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    2/15/2009, tsa. 25

    7/1/1998, tsa. 20

1 Akorinto 15:54

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 20:6; 21:4
  • +Yes 25:8

1 Akorinto 15:55

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ho 13:14

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2005, tsa. 29

    2/15/1995, tsa. 10

1 Akorinto 15:56

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Aro 6:23
  • +Aro 3:20; 7:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    11/15/2005, tsa. 29

    7/15/2000, tsa. 19

1 Akorinto 15:57

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yoh 3:16; Mac 4:12; 1Yo 5:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda,

    7/1/1998, tsa. 24

1 Akorinto 15:58

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Akl 1:23; Ahe 3:14; 2Pe 3:17
  • +Aro 12:11
  • +2Mb 15:7; 1Ak 3:8; Chv 14:13

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    12/2020, tsa. 13

    Nsanja ya Olonda (Yophunzira),

    1/2017, ptsa. 9-10

    Nsanja ya Olonda,

    5/15/2003, tsa. 22

    7/15/2000, tsa. 19

    7/1/1998, tsa. 24

    7/1/1992, ptsa. 28-29

    10/15/1989, tsa. 20

    Utumiki wa Ufumu,

    6/2000, tsa. 1

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

1 Akor. 15:1Aga 1:11
1 Akor. 15:1Mac 18:11
1 Akor. 15:1Aro 5:2
1 Akor. 15:2Aro 1:16
1 Akor. 15:2Aga 3:4
1 Akor. 15:3Aga 1:12
1 Akor. 15:3Sl 22:15; Yes 53:8, 12; Da 9:26; 1Pe 2:24
1 Akor. 15:4Yes 53:9; Mt 27:60
1 Akor. 15:4Mt 28:7
1 Akor. 15:4Lu 24:46
1 Akor. 15:4Sl 16:10; Yes 53:10; Yon 2:10
1 Akor. 15:5Lu 24:34
1 Akor. 15:5Yoh 20:26
1 Akor. 15:6Mt 28:17
1 Akor. 15:7Mac 12:17
1 Akor. 15:7Mac 1:2, 6
1 Akor. 15:8Mac 9:4; 1Ak 9:1
1 Akor. 15:9Aef 3:8
1 Akor. 15:9Mac 8:3; Aga 1:13; 1Ti 1:13
1 Akor. 15:10Aef 4:7
1 Akor. 15:102Ak 6:1
1 Akor. 15:102Ak 11:23
1 Akor. 15:10Afi 2:13
1 Akor. 15:11Mac 18:10
1 Akor. 15:12Mac 4:2; 17:31
1 Akor. 15:12Mt 22:23; Mac 26:8
1 Akor. 15:13Aro 10:7
1 Akor. 15:141At 4:14
1 Akor. 15:15Mac 3:15
1 Akor. 15:15Mac 1:22
1 Akor. 15:15Mac 2:24; 4:10; 13:30
1 Akor. 15:15Mac 17:31; 1Ak 6:14
1 Akor. 15:17Aro 4:25; Ahe 7:25
1 Akor. 15:18Mac 7:59
1 Akor. 15:181Ak 15:14
1 Akor. 15:19Yoh 1:12
1 Akor. 15:201Pe 1:3
1 Akor. 15:20Le 23:10; Akl 1:18
1 Akor. 15:20Mac 26:23
1 Akor. 15:21Ge 3:19
1 Akor. 15:21Yoh 11:25
1 Akor. 15:22Aro 5:12
1 Akor. 15:22Aro 5:17; 6:23
1 Akor. 15:23Chv 1:5
1 Akor. 15:23Mt 24:3; 25:31; 1At 4:16
1 Akor. 15:24Sl 110:2; Da 2:44
1 Akor. 15:25Sl 110:1
1 Akor. 15:26Chv 20:14
1 Akor. 15:27Sl 8:6; Aef 1:22
1 Akor. 15:27Ahe 2:8
1 Akor. 15:271Pe 3:22
1 Akor. 15:28Afi 3:21
1 Akor. 15:28Yoh 3:35; 14:28
1 Akor. 15:281Ak 3:23
1 Akor. 15:29Aro 6:4
1 Akor. 15:29Mac 17:31
1 Akor. 15:291Ak 12:13; Aga 3:27
1 Akor. 15:30Aro 8:36; 2Ak 11:26
1 Akor. 15:311Ak 4:9
1 Akor. 15:311At 2:19
1 Akor. 15:322Ak 1:8
1 Akor. 15:32Yes 22:13
1 Akor. 15:33Miy 13:20; 1Ak 5:6; 2Pe 2:2
1 Akor. 15:34Aro 13:11; Aef 5:14
1 Akor. 15:341At 4:5
1 Akor. 15:341Ak 6:5
1 Akor. 15:351Yo 3:2
1 Akor. 15:36Yoh 12:24
1 Akor. 15:37Ge 1:11
1 Akor. 15:38Ge 1:12
1 Akor. 15:381Ak 12:18
1 Akor. 15:39Ge 1:28
1 Akor. 15:40Ge 22:11; Da 7:10
1 Akor. 15:40Ge 2:7; Ahe 2:7
1 Akor. 15:40Mt 28:3; Lu 24:4
1 Akor. 15:41Sl 72:5
1 Akor. 15:41Ge 1:16
1 Akor. 15:41Da 12:3
1 Akor. 15:42Yoh 12:25
1 Akor. 15:42Aro 2:7
1 Akor. 15:43Yoh 17:14
1 Akor. 15:43Akl 3:4
1 Akor. 15:431Ak 1:27
1 Akor. 15:43Chv 20:4
1 Akor. 15:441Ak 6:13
1 Akor. 15:44Yoh 14:3
1 Akor. 15:45Ge 2:7
1 Akor. 15:451Ti 3:16
1 Akor. 15:45Yoh 5:26
1 Akor. 15:461Pe 3:18
1 Akor. 15:47Ge 3:19
1 Akor. 15:47Yoh 3:13; 6:33
1 Akor. 15:48Ge 2:7
1 Akor. 15:48Afi 3:20
1 Akor. 15:48Afi 3:21
1 Akor. 15:49Ge 5:3
1 Akor. 15:49Aro 8:29
1 Akor. 15:50Yoh 3:3
1 Akor. 15:501Pe 1:23
1 Akor. 15:511At 4:17
1 Akor. 15:521At 4:16
1 Akor. 15:53Aro 2:7
1 Akor. 15:53Aro 8:11; 2Ak 5:4
1 Akor. 15:54Chv 20:6; 21:4
1 Akor. 15:54Yes 25:8
1 Akor. 15:55Ho 13:14
1 Akor. 15:56Aro 6:23
1 Akor. 15:56Aro 3:20; 7:13
1 Akor. 15:57Yoh 3:16; Mac 4:12; 1Yo 5:4
1 Akor. 15:58Akl 1:23; Ahe 3:14; 2Pe 3:17
1 Akor. 15:58Aro 12:11
1 Akor. 15:582Mb 15:7; 1Ak 3:8; Chv 14:13
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
  • 9
  • 10
  • 11
  • 12
  • 13
  • 14
  • 15
  • 16
  • 17
  • 18
  • 19
  • 20
  • 21
  • 22
  • 23
  • 24
  • 25
  • 26
  • 27
  • 28
  • 29
  • 30
  • 31
  • 32
  • 33
  • 34
  • 35
  • 36
  • 37
  • 38
  • 39
  • 40
  • 41
  • 42
  • 43
  • 44
  • 45
  • 46
  • 47
  • 48
  • 49
  • 50
  • 51
  • 52
  • 53
  • 54
  • 55
  • 56
  • 57
  • 58
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
1 Akorinto 15:1-58

1 Akorinto

15 Tsopano abale, ndikukuuzani uthenga wabwino+ umene ndinaulengeza kwa inu,+ umenenso munaulandira, ndiponso umene mwakhazikikamo.+ 2 Mukupulumutsidwa+ ndi uthenga wabwino umenewo ngati mwaugwiritsitsa. Popanda kutero, ndiye kuti munakhala okhulupirira pachabe,+ malinga ndi mawu amene ndinakuuzani polengeza uthengawo kwa inu.

3 Mwa zinthu zofunika kwambiri zimene ndinakupatsirani zija, zimenenso ineyo ndinalandira,+ panali zonena kuti, Khristu anafera machimo athu, malinga ndi Malemba.+ 4 Ndiponso kuti anaikidwa m’manda,+ kenako anaukitsidwa+ tsiku lachitatu,+ mogwirizana ndi Malemba.+ 5 Panalinso zoti anaonekera kwa Kefa,+ kenako kwa atumwi 12+ aja. 6 Ndiyeno anaonekeranso kwa abale oposa 500 pa nthawi imodzi, ndipo ambiri a iwo akali ndi moyo mpaka lero,+ koma ena anagona mu imfa. 7 Kenako anaonekera kwa Yakobo,+ kenakonso kwa atumwi onse.+ 8 Koma pomalizira pake anaonekera kwa ine,+ ngati khanda lobadwa masiku asanakwane.

9 Ineyo ndine wamng’ono kwambiri+ mwa atumwi onse, ndipo si ine woyenera kutchedwa mtumwi, chifukwa ndinazunza+ mpingo wa Mulungu. 10 Koma mwa kukoma mtima kwakukulu+ kwa Mulungu, ndili monga ndililimu. Ndipo kukoma mtima kwake kwakukulu kumene anandisonyeza sikunapite pachabe,+ koma ndinagwira ntchito molimbika kuposa atumwi ena onse.+ Ngakhale zili choncho, si mwa ine ndekha ayi, koma kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu kumene kuli nane.+ 11 Komabe, kaya ndi ineyo kapena iwowo, zimene tikulalikira ndi zomwezo, zimenenso mwazikhulupirirazo.+

12 Tsopano ngati timalalikira kuti Khristu anaukitsidwa kwa akufa,+ bwanji ena mwa inu akunena kuti akufa sadzaukitsidwa?+ 13 Chifukwa ngati akufa sadzauka, ndiye kuti Khristu nayenso sanauke.+ 14 Koma ngati Khristu sanauke, kulalikira kwathu n’kopanda pake, ndipo chikhulupiriro chathu n’chopanda pake.+ 15 Ndiponso, ndiye kuti ifenso takhala mboni zonama za Mulungu,+ chifukwa tachita umboni+ wonamizira Mulungu kuti anaukitsa Khristu+ pamene sanamuukitse, ngati akufa sadzaukadi.+ 16 Pakuti ngati akufa sadzauka, Khristunso sanauke. 17 Ndipo ngati Khristu sanauke, chikhulupiriro chanu chilibe ntchito ndipo mukadali m’machimo anu.+ 18 Ndiye kutinso anthu amene anagona mu imfa mwa Khristu,+ kutha kwawo kunali komweko.+ 19 Ngati tayembekezera Khristu+ m’moyo uno wokha, ndiye kuti ndife omvetsa chisoni kuposa anthu ena onse.

20 Komabe, Khristu anaukitsidwa kwa akufa,+ n’kukhala chipatso choyambirira+ cha amene akugona mu imfa.+ 21 Popeza imfa+ inafika kudzera mwa munthu mmodzi, kuuka+ kwa akufa kunafikanso kudzera mwa munthu mmodzi. 22 Pakuti monga mwa Adamu onse akufa,+ momwemonso mwa Khristu onse adzapatsidwa+ moyo. 23 Koma aliyense pamalo pake: Choyamba Khristu, amene ndi chipatso choyambirira,+ kenako ake a Khristu pa nthawi ya kukhalapo*+ kwake. 24 Ndiyeno pa mapeto pake, adzapereka ufumu kwa Mulungu wake ndi Atate wake, atathetsa maboma onse, ulamuliro wonse, ndi mphamvu zonse.+ 25 Pakuti ayenera kulamulira monga mfumu kufikira Mulungu ataika adani onse pansi pa mapazi+ ake. 26 Imfa nayonso, monga mdani womalizira, idzawonongedwa.+ 27 Pakuti Mulungu “anaika zinthu zonse pansi pa mapazi ake.”+ Koma pamene akunena kuti ‘waika zinthu zonse pansi pake,’+ n’zodziwikiratu kuti sakuphatikizapo amene anaika zinthu zonsezo pansi pa iye.+ 28 Koma zinthu zonse zikadzakhala pansi pake,+ Mwanayonso adzadziika pansi pa amene+ anaika zinthu zonse pansi pake, kuti Mulungu akhale zinthu zonse kwa aliyense.+

29 Apo ayi, kodi amene akubatizidwa kuti akhale akufa adzatani?+ Ngati akufa sadzauka,+ n’chifukwa chiyani anthuwo akubatizidwa+ kuti akhale akufa? 30 Kodi ifeyo tikuikiranji moyo wathu pachiswe nthawi zonse?+ 31 Tsiku ndi tsiku ndimakhala pa ngozi yoti ndikhoza kufa.+ Ndikukutsimikizirani zimenezi ndili wokondwera nanu,+ abale, kukondwera kumene ndili nako mwa Khristu Yesu Ambuye wathu. 32 Ngati ndinamenyana ndi zilombo ku Efeso+ monga ena anachitira, ndinapindulapo chiyani? Ngati akufa sadzauka, “tiyeni tidye ndi kumwa, pakuti mawa tifa.”+ 33 Musasocheretsedwe. Kugwirizana ndi anthu oipa kumawononga makhalidwe abwino.+ 34 Dzukani ku tulo tanu+ kuti mukhale olungama ndipo musamachite tchimo, pakuti ena sadziwa Mulungu.+ Ndikulankhula zimenezi kuti muchite manyazi.+

35 Ngakhale zili choncho, wina anganene kuti: “Kodi akufa adzaukitsidwa motani? Inde, kodi iwo adzauka ndi thupi lotani?”+ 36 Wopusa iwe! Chimene wabzala sichikhala ndi moyo pokhapokha chitafa kaye.+ 37 Ndipo chimene wafesa si mmera umene umakulawo, koma mbewu chabe,+ kaya ya tirigu kapena ina iliyonse. 38 Koma Mulungu amaipatsa thupi+ monga mwa kufuna kwake,+ ndipo mbewu iliyonse amaipatsa thupi lake. 39 Mnofu sukhala wa mtundu umodzi, koma pali mnofu wa munthu, ndipo pali wa nyama, palinso wa mbalame, ndi winanso wa nsomba.+ 40 Palinso matupi akumwamba,+ ndi matupi+ apadziko lapansi, koma ulemerero+ wa matupi akumwamba ndi wina, ndipo ulemerero wa matupi apadziko lapansi ndi winanso. 41 Ulemerero wa dzuwa+ ndi wosiyana ndi ulemerero wa mwezi,+ ndipo ulemerero wa nyenyezi ndi winanso. Ngakhale ulemerero wa nyenyezi+ ina, umasiyana ndi ulemerero wa inzake.

42 Ndi mmenenso zilili ndi kuuka kwa akufa.+ Thupi limafesedwa lili lokhoza kuwonongeka, limaukitsidwa losakhoza kuwonongeka.+ 43 Limafesedwa lonyozeka,+ limaukitsidwa mu ulemerero.+ Limafesedwa lofooka,+ limaukitsidwa mu mphamvu.+ 44 Limafesedwa thupi lanyama,+ limaukitsidwa thupi lauzimu.+ Ngati pali thupi lanyama, palinso lauzimu. 45 Zinachita kulembedwa kuti: “Munthu woyambirira, Adamu, anakhala munthu wamoyo.”+ Adamu womalizira anakhala mzimu+ wopatsa moyo.+ 46 Ngakhale zili choncho, choyambacho si chauzimu ayi koma chamnofu. Kenako panabwera chauzimu.+ 47 Munthu woyambayo anachokera padziko lapansi ndipo anapangidwa ndi fumbi.+ Wachiwiriyo anachokera kumwamba.+ 48 Mmene wopangidwa ndi fumbiyo alili,+ ndi mmenenso opangidwa ndi fumbiwo alili. Ndipo mmene wakumwambayo alili,+ ndi mmenenso akumwambawo alili.+ 49 Ndiponso, monga tilili m’chifaniziro+ cha wopangidwa ndi fumbi uja, tidzakhalanso m’chifaniziro+ cha wakumwambayo.

50 Koma abale, ndikunenetsa kuti mnofu ndi magazi sizingalowe ufumu wa Mulungu.+ Komanso chowonongeka sichingalandire kusawonongeka.+ 51 Tamverani! Ndikukuuzani chinsinsi chopatulika: Si tonse amene tidzagona mu imfa, koma tonse tidzasandulika,+ 52 m’kamphindi, m’kuphethira kwa diso, pa kulira kwa lipenga lomaliza. Pakuti lipengalo+ lidzalira, ndipo akufa adzaukitsidwa osakhoza kuwonongeka, ndipo tidzasandulika. 53 Pakuti chokhoza kuwonongekachi chidzavala kusawonongeka,+ ndipo chokhoza kufachi+ chidzavala kusafa. 54 Koma chokhoza kuwonongekachi chikadzavala kusawonongeka, ndipo chokhoza kufachi chikadzavala kusafa, pamenepo adzakwaniritsidwa mawu amene analembedwa kuti: “Imfa+ yamezedwa kwamuyaya.”+ 55 “Imfa iwe, kupambana kwako kuli kuti? Imfawe, mphamvu yako ili kuti?”+ 56 Mphamvu+ imene imabala imfa ndiyo uchimo, koma mphamvu ya uchimo ndi Chilamulo.+ 57 Koma Mulungu ayamikike, pakuti amatithandiza kuti tipambane kudzera mwa Ambuye wathu Yesu Khristu.+

58 Choncho abale anga okondedwa, khalani olimba,+ osasunthika, okhala ndi zochita zambiri nthawi zonse mu ntchito ya Ambuye,+ podziwa kuti zonse zimene mukuchita mu ntchito ya Ambuye sizidzapita pachabe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena