1 Mafumu 16:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako anagula phiri la Samariya* kwa Semeri ndi matalente* awiri a siliva. Ndiyeno anayamba kumanga mzinda paphiripo n’kuutcha dzina la Semeri mbuye wa phirilo, loti Samariya.+ 1 Mafumu 16:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ahabu mwana wa Omuri anakhala mfumu ya Isiraeli m’chaka cha 38 cha Asa mfumu ya Yuda. Iye analamulira Isiraeli ku Samariya+ zaka 22.
24 Kenako anagula phiri la Samariya* kwa Semeri ndi matalente* awiri a siliva. Ndiyeno anayamba kumanga mzinda paphiripo n’kuutcha dzina la Semeri mbuye wa phirilo, loti Samariya.+
29 Ahabu mwana wa Omuri anakhala mfumu ya Isiraeli m’chaka cha 38 cha Asa mfumu ya Yuda. Iye analamulira Isiraeli ku Samariya+ zaka 22.