1 Mafumu 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Solomo anamanganso Gezeri, Beti-horoni Wakumunsi,+ 2 Mbiri 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno anamanga mzinda wa Beti-horoni Wakumtunda+ ndi Beti-horoni Wakumunsi.+ Imeneyi inali mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri,+ zitseko ndi mipiringidzo.+
5 Ndiyeno anamanga mzinda wa Beti-horoni Wakumtunda+ ndi Beti-horoni Wakumunsi.+ Imeneyi inali mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri,+ zitseko ndi mipiringidzo.+