2 Mbiri 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Amaziya analimba mtima n’kutsogolera anthu ake kupita kuchigwa cha Mchere.+ Kumeneko anapha ana a Seiri+ okwana 10,000.+
11 Ndiyeno Amaziya analimba mtima n’kutsogolera anthu ake kupita kuchigwa cha Mchere.+ Kumeneko anapha ana a Seiri+ okwana 10,000.+