2 Mafumu 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pankhondoyo, Ayuda anagonja pamaso pa Aisiraeli+ moti aliyense anathawira kuhema wake.