1 Mafumu 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndikupatsanso zomwe sunapemphe,+ chuma+ ndi ulemerero, moti sikudzakhalanso mfumu ngati iwe masiku ako onse.+ Salimo 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Munthu ameneyo adzakhala ngati mtengo wobzalidwa m’mphepete mwa mitsinje ya madzi,+Umene umabala zipatso m’nyengo yake,+Umenenso masamba ake safota,+Ndipo zochita zake zonse zidzamuyendera bwino.+ Miyambo 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Madalitso a Yehova ndi amene amalemeretsa,+ ndipo sawonjezerapo ululu.+
13 Ndikupatsanso zomwe sunapemphe,+ chuma+ ndi ulemerero, moti sikudzakhalanso mfumu ngati iwe masiku ako onse.+
3 Munthu ameneyo adzakhala ngati mtengo wobzalidwa m’mphepete mwa mitsinje ya madzi,+Umene umabala zipatso m’nyengo yake,+Umenenso masamba ake safota,+Ndipo zochita zake zonse zidzamuyendera bwino.+