Oweruza 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno patapita nthawi, ana a Amoni anayamba kumenyana ndi Aisiraeli.+ 2 Samueli 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pambuyo pake, mfumu ya ana a Amoni+ inamwalira, ndipo Hanuni mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwa bambo ake.+ 2 Mbiri 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pambuyo pake ana a Mowabu,+ ana a Amoni,+ pamodzi ndi Aamonimu+ ena, anabwera kudzamenyana ndi Yehosafati.+ Yeremiya 49:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ponena za ana a Amoni+ Yehova wanena kuti: “Kodi Isiraeli alibe ana aamuna, kapena kodi alibe wolandira cholowa? N’chifukwa chiyani Malikamu+ watenga Gadi+ kukhala cholowa chake? N’chifukwa chiyani anthu olambira Malikamu akukhala m’mizinda ya Isiraeli?”+
10 Pambuyo pake, mfumu ya ana a Amoni+ inamwalira, ndipo Hanuni mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwa bambo ake.+
20 Pambuyo pake ana a Mowabu,+ ana a Amoni,+ pamodzi ndi Aamonimu+ ena, anabwera kudzamenyana ndi Yehosafati.+
49 Ponena za ana a Amoni+ Yehova wanena kuti: “Kodi Isiraeli alibe ana aamuna, kapena kodi alibe wolandira cholowa? N’chifukwa chiyani Malikamu+ watenga Gadi+ kukhala cholowa chake? N’chifukwa chiyani anthu olambira Malikamu akukhala m’mizinda ya Isiraeli?”+