Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 28:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Davide anasonkhanitsa akalonga onse+ a Isiraeli ku Yerusalemu. Akalongawo+ anali a mafuko ndi a magulu otumikira mfumu, atsogoleri a magulu a anthu 1,000,+ atsogoleri a magulu a anthu 100,+ ndiponso atsogoleri oyang’anira katundu yense+ ndi ziweto+ za mfumu ndi za ana ake.+ Panalinso nduna za panyumba ya mfumu+ ndi amuna amphamvu,+ ngakhale mwamuna aliyense wamphamvu ndi wolimba mtima.

  • Mlaliki 12:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Mawu a anthu anzeru ali ngati zisonga zobayira ng’ombe pozitsogolera,+ ndipo anthu amene amadzipereka kusonkhanitsa mawu anzeru, ali ngati misomali yokhomerera kwambiri.+ Mawuwo aperekedwa ndi m’busa mmodzi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena