2 Mafumu 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 M’chaka chachitatu cha Hoshiya+ mwana wa Ela mfumu ya Isiraeli, Hezekiya+ mwana wa Ahazi,+ mfumu ya Yuda anakhala mfumu. Mateyu 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Hezekiya anabereka Manase.+Manase+ anabereka Amoni.+Amoni+ anabereka Yosiya.
18 M’chaka chachitatu cha Hoshiya+ mwana wa Ela mfumu ya Isiraeli, Hezekiya+ mwana wa Ahazi,+ mfumu ya Yuda anakhala mfumu.