2 Mbiri 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano ineyo ndikufunitsitsa mumtima mwanga kuchita pangano+ ndi Yehova Mulungu wa Isiraeli, kuti mkwiyo wake umene watiyakira utichokere. Salimo 78:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Anawasonyeza mkwiyo wake woyaka moto,+Ukali, ziweruzo zamphamvu ndi masautso.+Anawatumizira makamu a angelo obweretsa masoka.+
10 Tsopano ineyo ndikufunitsitsa mumtima mwanga kuchita pangano+ ndi Yehova Mulungu wa Isiraeli, kuti mkwiyo wake umene watiyakira utichokere.
49 Anawasonyeza mkwiyo wake woyaka moto,+Ukali, ziweruzo zamphamvu ndi masautso.+Anawatumizira makamu a angelo obweretsa masoka.+