Numeri 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Munthu wina aliyense mwa inu kapena mwa mbadwa zanu, amene wadetsedwa pokhudza mtembo wa munthu,+ kapena amene ali pa ulendo wautali, akonzebe nsembe ya pasika yopereka kwa Yehova. Numeri 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Azikonza nsembeyo m’mwezi wachiwiri+ pa tsiku la 14, madzulo kuli kachisisira. Azidya nyama ya nsembeyo pamodzi ndi mikate yopanda chofufumitsa, ndiponso masamba owawa.+
10 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Munthu wina aliyense mwa inu kapena mwa mbadwa zanu, amene wadetsedwa pokhudza mtembo wa munthu,+ kapena amene ali pa ulendo wautali, akonzebe nsembe ya pasika yopereka kwa Yehova.
11 Azikonza nsembeyo m’mwezi wachiwiri+ pa tsiku la 14, madzulo kuli kachisisira. Azidya nyama ya nsembeyo pamodzi ndi mikate yopanda chofufumitsa, ndiponso masamba owawa.+