2 Mbiri 30:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma mfumuyo, akalonga ake+ ndi mpingo wonse+ ku Yerusalemu anagwirizana zoti achite pasikayo m’mwezi wachiwiri.+ 2 Mbiri 30:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Atatero anapha nyama ya pasika+ pa tsiku la 14 la mwezi wachiwiri. Ansembe ndi Alevi anali atachititsidwa manyazi moti anadziyeretsa+ n’kubweretsa nsembe zopsereza kunyumba ya Yehova.
2 Koma mfumuyo, akalonga ake+ ndi mpingo wonse+ ku Yerusalemu anagwirizana zoti achite pasikayo m’mwezi wachiwiri.+
15 Atatero anapha nyama ya pasika+ pa tsiku la 14 la mwezi wachiwiri. Ansembe ndi Alevi anali atachititsidwa manyazi moti anadziyeretsa+ n’kubweretsa nsembe zopsereza kunyumba ya Yehova.