Nehemiya 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno ndinazindikira kuti magawo+ a Alevi sanali kuperekedwa kwa iwo, moti aliyense wa Aleviwo ndi oimba amene anali kutumikira anathawa ndipo anapita kumunda wake.+ 1 Akorinto 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti m’chilamulo cha Mose muli mawu akuti: “Usamange ng’ombe pakamwa pamene ikupuntha mbewu.”+ Kodi ndi ng’ombe zimene Mulungu akusamalira?
10 Ndiyeno ndinazindikira kuti magawo+ a Alevi sanali kuperekedwa kwa iwo, moti aliyense wa Aleviwo ndi oimba amene anali kutumikira anathawa ndipo anapita kumunda wake.+
9 Pakuti m’chilamulo cha Mose muli mawu akuti: “Usamange ng’ombe pakamwa pamene ikupuntha mbewu.”+ Kodi ndi ng’ombe zimene Mulungu akusamalira?