Yoswa 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mizinda yonse ya ansembe, ana a Aroni,+ inalipo 13 ndi malo ake odyetserako ziweto.+