2 Mbiri 31:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Hezekiya anachita zimenezi mu Yuda yense, ndipo anapitiriza kuchita zabwino,+ zoyenera+ ndi zokhulupirika+ pamaso pa Yehova Mulungu wake. 2 Mbiri 31:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anagwira ndi mtima wake wonse+ ntchito iliyonse imene anaiyamba mu utumiki+ wa panyumba ya Mulungu woona ndi m’chilamulo,+ pofunafuna+ Mulungu wake, ndipo zinthu zinamuyendera bwino.+
20 Hezekiya anachita zimenezi mu Yuda yense, ndipo anapitiriza kuchita zabwino,+ zoyenera+ ndi zokhulupirika+ pamaso pa Yehova Mulungu wake.
21 Anagwira ndi mtima wake wonse+ ntchito iliyonse imene anaiyamba mu utumiki+ wa panyumba ya Mulungu woona ndi m’chilamulo,+ pofunafuna+ Mulungu wake, ndipo zinthu zinamuyendera bwino.+