Yesaya 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Milungu yopanda phindu idzatheratu.+ Ezekieli 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “‘Munthu woipa akabwerera, kusiya machimo ake onse amene anali kuchita+ ndipo akasunga malamulo anga onse n’kuchita zinthu motsatira malamulo ndiponso mwachilungamo,+ adzakhalabe ndi moyo. Sadzafa ayi.+ Hoseya 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Dziko la Asuri silidzatipulumutsa.+ Ife sitidzakwera pamahatchi.+ Sitidzauzanso ntchito ya manja athu kuti: “Inu Mulungu wathu!” chifukwa inu mumachitira chifundo mwana wamasiye.’*+ Mateyu 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyetu mubale zipatso zosonyeza kulapa.+
21 “‘Munthu woipa akabwerera, kusiya machimo ake onse amene anali kuchita+ ndipo akasunga malamulo anga onse n’kuchita zinthu motsatira malamulo ndiponso mwachilungamo,+ adzakhalabe ndi moyo. Sadzafa ayi.+
3 Dziko la Asuri silidzatipulumutsa.+ Ife sitidzakwera pamahatchi.+ Sitidzauzanso ntchito ya manja athu kuti: “Inu Mulungu wathu!” chifukwa inu mumachitira chifundo mwana wamasiye.’*+