1 Samueli 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 (Kalekale mu Isiraeli, munthu akafuna kukafunsira kwa Mulungu ankanena kuti: “Tiyeni tipite kwa wamasomphenya.”*+ Pakuti amene amatchedwa mneneri masiku ano, kalekalelo anali kutchedwa kuti wamasomphenya.) Yesaya 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti Yehova wakukhuthulirani mzimu wa tulo tatikulu+ ndipo watseka maso anu, omwe ndi aneneri.+ Waphimba mitu yanu,+ imene ndi anthu amasomphenya.+
9 (Kalekale mu Isiraeli, munthu akafuna kukafunsira kwa Mulungu ankanena kuti: “Tiyeni tipite kwa wamasomphenya.”*+ Pakuti amene amatchedwa mneneri masiku ano, kalekalelo anali kutchedwa kuti wamasomphenya.)
10 Pakuti Yehova wakukhuthulirani mzimu wa tulo tatikulu+ ndipo watseka maso anu, omwe ndi aneneri.+ Waphimba mitu yanu,+ imene ndi anthu amasomphenya.+