-
2 Mbiri 33:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Nkhani zokhudza pemphero lake,+ zokhudza mmene Mulungu anamvera kupembedza kwake,+ machimo ake onse,+ ndi kusakhulupirika kwake+ zinalembedwa m’mawu a amasomphenya ake. M’mawu amenewa munalembedwanso nkhani zokhudza malo amene iye anamangako malo okwezeka+ n’kuikapo mizati yopatulika+ ndi zifaniziro zogoba+ asanadzichepetse.+
-