2 Mafumu 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 M’chaka cha 18 cha Mfumu Yosiya, mfumuyo inatuma Safani+ mwana wa Azaliya mwana wa Mesulamu yemwe anali mlembi, kuti apite kunyumba ya Yehova. Inam’tuma ndi mawu akuti:
3 M’chaka cha 18 cha Mfumu Yosiya, mfumuyo inatuma Safani+ mwana wa Azaliya mwana wa Mesulamu yemwe anali mlembi, kuti apite kunyumba ya Yehova. Inam’tuma ndi mawu akuti: