2 Mafumu 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aziperekenso kwa amisiri, kwa omanga nyumba, ndi kwa amisiri omanga ndi miyala, komanso agulire matabwa ndi miyala yosema kuti akonzere nyumbayo.+
6 Aziperekenso kwa amisiri, kwa omanga nyumba, ndi kwa amisiri omanga ndi miyala, komanso agulire matabwa ndi miyala yosema kuti akonzere nyumbayo.+