2 Mafumu 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako Safani mlembi anauza mfumuyo kuti: “Pali buku+ limene wansembe Hilikiya wandipatsa.” Ndiyeno Safani anayamba kuwerenga bukulo pamaso pa mfumu.
10 Kenako Safani mlembi anauza mfumuyo kuti: “Pali buku+ limene wansembe Hilikiya wandipatsa.” Ndiyeno Safani anayamba kuwerenga bukulo pamaso pa mfumu.