Ekisodo 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mwamsanga, Mose anaitana akulu onse a Isiraeli+ ndi kuwauza kuti: “Sankhani nkhosa ndi mbuzi* malinga ndi mabanja anu, muiphere nsembe ya pasika.+ 1 Akorinto 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotsani chofufumitsa chakalecho, kuti mukhale mtanda watsopano,+ popeza ndinu opanda chofufumitsa. Pakuti Khristu+ waperekedwa+ monga nsembe yathu ya pasika.+
21 Mwamsanga, Mose anaitana akulu onse a Isiraeli+ ndi kuwauza kuti: “Sankhani nkhosa ndi mbuzi* malinga ndi mabanja anu, muiphere nsembe ya pasika.+
7 Chotsani chofufumitsa chakalecho, kuti mukhale mtanda watsopano,+ popeza ndinu opanda chofufumitsa. Pakuti Khristu+ waperekedwa+ monga nsembe yathu ya pasika.+