Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 9:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Tsopano ana a Isiraeli akonze nsembe ya pasika+ pa nthawi yake yoikidwiratu.+

  • Yoswa 5:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ana a Isiraeliwo anakhalabe ku Giligala. Anachita pasika madzulo pa tsiku la 14 la mweziwo,+ ali m’chipululu cha Yeriko.

  • 2 Mafumu 23:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Tsopano mfumuyo inalamula anthu onse kuti: “Chitirani pasika+ Yehova Mulungu wanu, malinga ndi zimene zalembedwa m’buku la panganoli.”+

  • 2 Mbiri 35:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Muphe nyama ya pasika+ n’kudziyeretsa+ ndipo muikonzere abale anu kuti muchite mogwirizana ndi mawu a Yehova kudzera mwa Mose.”+

  • Ezara 6:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Chifukwa chakuti ansembe ndi Alevi anadziyeretsa+ monga gulu limodzi, onse anali oyera. Choncho Aleviwo anapha nyama ya pasika+ ya anthu onse amene anachokera ku ukapolo, ya abale awo ansembe, ndiponso yawo.

  • Luka 22:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Tsopano tsiku la chikondwerero cha mikate yopanda chofufumitsa linafika, tsiku loyenera kupha nyama yoperekera nsembe ya pasika.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena