Numeri 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi amuna inu mukuyesa n’chinthu chaching’ono kuti Mulungu wa Isiraeli anakupatulani+ pakati pa Aisiraeli, n’kukutengani kukhala akeake, kuti muzitumikira Yehova pachihema chake ndi kutumikira khamulo?+ Salimo 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tumikirani Yehova mwamantha.+Kondwerani ndipo nthunthumirani.+ Salimo 100:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tumikirani Yehova mokondwera.+Bwerani kwa iye mukufuula mosangalala.+ Tito 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ine Paulo, kapolo+ wa Mulungu ndi mtumwi+ wa Yesu Khristu, ndili ndi chikhulupiriro chogwirizana ndi cha anthu osankhidwa+ ndi Mulungu. Komanso ndine wodziwa molondola+ choonadi+ chokhudza kudzipereka kwathu kwa Mulungu,+
9 Kodi amuna inu mukuyesa n’chinthu chaching’ono kuti Mulungu wa Isiraeli anakupatulani+ pakati pa Aisiraeli, n’kukutengani kukhala akeake, kuti muzitumikira Yehova pachihema chake ndi kutumikira khamulo?+
1 Ine Paulo, kapolo+ wa Mulungu ndi mtumwi+ wa Yesu Khristu, ndili ndi chikhulupiriro chogwirizana ndi cha anthu osankhidwa+ ndi Mulungu. Komanso ndine wodziwa molondola+ choonadi+ chokhudza kudzipereka kwathu kwa Mulungu,+