2 Mafumu 23:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti pasika ngati ameneyu anali asanachitikepo kuyambira masiku a oweruza amene anaweruza Isiraeli,+ ngakhalenso masiku onse a mafumu a Isiraeli ndi mafumu a Yuda.+
22 Pakuti pasika ngati ameneyu anali asanachitikepo kuyambira masiku a oweruza amene anaweruza Isiraeli,+ ngakhalenso masiku onse a mafumu a Isiraeli ndi mafumu a Yuda.+