-
Mlaliki 8:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Pali chinthu china chachabe chimene chimachitika padziko lapansi: Pali anthu olungama amene amakumana ndi zinthu zimene amayenera kukumana nazo anthu oipa,+ ndiponso pali anthu oipa amene amakumana ndi zinthu zimene amayenera kukumana nazo anthu olungama.+ Ndinanena kuti zimenezinso n’zachabechabe.
-