-
1 Mafumu 14:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Choncho anamuika m’manda ndipo Aisiraeli onse anamulira, mogwirizana ndi mawu a Yehova amene analankhula kudzera mwa mtumiki wake, mneneri Ahiya.
-