2 Mafumu 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nkhani zina zokhudza Yehoyakimu+ ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Yuda. 2 Mbiri 35:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 ndiponso zochita zake, zoyambirira ndi zomalizira,+ zinalembedwa m’Buku+ la Mafumu a Isiraeli ndi Yuda.
5 Nkhani zina zokhudza Yehoyakimu+ ndi zonse zimene anachita, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Yuda.
27 ndiponso zochita zake, zoyambirira ndi zomalizira,+ zinalembedwa m’Buku+ la Mafumu a Isiraeli ndi Yuda.