2 Mbiri 36:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nkhani zina+ zokhudza Yehoyakimu ndi zonyansa+ zimene anachita, ndiponso zoipa zimene zinapezedwa zokhudza iye, zinalembedwa m’Buku+ la Mafumu a Isiraeli ndi Yuda. Kenako Yehoyakini+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
8 Nkhani zina+ zokhudza Yehoyakimu ndi zonyansa+ zimene anachita, ndiponso zoipa zimene zinapezedwa zokhudza iye, zinalembedwa m’Buku+ la Mafumu a Isiraeli ndi Yuda. Kenako Yehoyakini+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.