Ekisodo 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho Mose ndi Aroni anapita kwa Farao ndi kumuuza kuti: “Yehova Mulungu wa Aheberi wanena kuti, ‘Udzakana kundigonjera kufikira liti?+ Lola anthu anga apite kuti akanditumikire. 2 Mbiri 32:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Komabe, Hezekiya anadzichepetsa+ pambuyo pa kudzikuza kwa mtima wake. Anadzichepetsa limodzi ndi anthu a ku Yerusalemu, ndipo mkwiyo wa Yehova sunawagwere m’masiku a Hezekiya.+ Danieli 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Koma inuyo a Belisazara,+ amene ndinu mwana wake, simunadzichepetse mumtima mwanu+ ngakhale kuti munali kudziwa zonsezi.+ Yakobo 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Dzichepetseni pamaso pa Yehova,+ ndipo iye adzakukwezani.+ 1 Petulo 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho dzichepetseni pansi pa dzanja lamphamvu la Mulungu, kuti adzakukwezeni m’nthawi yake.+
3 Choncho Mose ndi Aroni anapita kwa Farao ndi kumuuza kuti: “Yehova Mulungu wa Aheberi wanena kuti, ‘Udzakana kundigonjera kufikira liti?+ Lola anthu anga apite kuti akanditumikire.
26 Komabe, Hezekiya anadzichepetsa+ pambuyo pa kudzikuza kwa mtima wake. Anadzichepetsa limodzi ndi anthu a ku Yerusalemu, ndipo mkwiyo wa Yehova sunawagwere m’masiku a Hezekiya.+
22 “Koma inuyo a Belisazara,+ amene ndinu mwana wake, simunadzichepetse mumtima mwanu+ ngakhale kuti munali kudziwa zonsezi.+