Salimo 86:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, ndilangizeni za njira yanu.+Ndidzayenda m’choonadi chanu.+Ndipatseni mtima wosagawanika kuti ndiope dzina lanu.+ Salimo 119:102 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 102 Sindinapatuke pa zigamulo zanu,+Pakuti inu mwandilangiza.+ Yesaya 30:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Yehova adzakupatsani masautso kuti akhale chakudya chanu, ndiponso adzakupatsani kuponderezedwa kuti kukhale madzi anu akumwa.+ Koma Mlangizi wako Wamkulu adzasiya kudzibisa ndipo maso ako adzayamba kuona Mlangizi wako Wamkulu.+ Yesaya 54:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ana ako onse+ adzakhala anthu ophunzitsidwa ndi Yehova,+ ndipo mtendere wa ana ako udzakhala wochuluka.+
11 Inu Yehova, ndilangizeni za njira yanu.+Ndidzayenda m’choonadi chanu.+Ndipatseni mtima wosagawanika kuti ndiope dzina lanu.+
20 Yehova adzakupatsani masautso kuti akhale chakudya chanu, ndiponso adzakupatsani kuponderezedwa kuti kukhale madzi anu akumwa.+ Koma Mlangizi wako Wamkulu adzasiya kudzibisa ndipo maso ako adzayamba kuona Mlangizi wako Wamkulu.+
13 Ana ako onse+ adzakhala anthu ophunzitsidwa ndi Yehova,+ ndipo mtendere wa ana ako udzakhala wochuluka.+