Deuteronomo 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma asadzichulukitsire mahatchi+ kapena kuchititsa anthu kubwerera ku Iguputo kuti akakhale ndi mahatchi ochuluka+ pakuti Yehova wakuuzani kuti, ‘Musabwererenso kudzera njira iyi.’ 2 Mbiri 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Panalinso mahatchi amene Solomo anali kugula kuchokera ku Iguputo,+ ndipo gulu la amalonda a mfumu ndilo linali kugula mahatchiwo m’magulumagulu.+
16 Koma asadzichulukitsire mahatchi+ kapena kuchititsa anthu kubwerera ku Iguputo kuti akakhale ndi mahatchi ochuluka+ pakuti Yehova wakuuzani kuti, ‘Musabwererenso kudzera njira iyi.’
16 Panalinso mahatchi amene Solomo anali kugula kuchokera ku Iguputo,+ ndipo gulu la amalonda a mfumu ndilo linali kugula mahatchiwo m’magulumagulu.+