2 Mbiri 9:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Anthu anali kubweretsa mahatchi+ kwa Solomo kuchokera ku Iguputo+ ndi mayiko ena onse.