Miyambo 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 mukungonyalanyaza malangizo anga onse,+ ndipo simunamvere kudzudzula kwanga,+ Miyambo 19:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mvera uphungu+ ndipo utsatire malangizo* kuti udzakhale wanzeru m’tsogolo.+ Mlaliki 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Komanso, m’njira iliyonse imene munthu wopusa amayenda,+ mtima wake umakhala wopanda nzeru, ndipo amauza aliyense kuti ndi wopusa.+ Yesaya 30:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Yehova wanena kuti: “Tsoka kwa ana aamuna osamva,+ amene amakonda kuchita zofuna zawo osati zofuna zanga,+ amene amapanga mgwirizano mwa kuthira pansi chakumwa monga nsembe motsutsana ndi zofuna zanga,* kuti awonjezere tchimo pa tchimo,+
3 Komanso, m’njira iliyonse imene munthu wopusa amayenda,+ mtima wake umakhala wopanda nzeru, ndipo amauza aliyense kuti ndi wopusa.+
30 Yehova wanena kuti: “Tsoka kwa ana aamuna osamva,+ amene amakonda kuchita zofuna zawo osati zofuna zanga,+ amene amapanga mgwirizano mwa kuthira pansi chakumwa monga nsembe motsutsana ndi zofuna zanga,* kuti awonjezere tchimo pa tchimo,+