Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 1:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 Solomo mwana wa Davide anapitiriza kukhala wamphamvu mu ufumu wake.+ Yehova Mulungu wake anali naye,+ ndipo anapitiriza kumukulitsa kuposa wina aliyense.+

  • 2 Mbiri 7:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Iweyo ukayenda pamaso panga monga momwe Davide+ bambo ako anayendera, mwa kuchita zonse zimene ndakulamula+ ndi kusunga malangizo anga+ ndi zigamulo zanga,+

  • 2 Mbiri 8:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Anapereka nsembezo mogwirizana ndi dongosolo la tsiku ndi tsiku+ loperekera nsembe, malinga ndi chilamulo cha Mose. Nsembezo zinali za pa masabata,+ za pa masiku okhala mwezi,+ ndi za pa zikondwerero zoikidwiratu+ zochitika katatu pa chaka.+ Zikondwererozo zinali chikondwerero cha mikate yopanda chofufumitsa,+ chikondwerero cha masabata,+ ndi chikondwerero cha misasa.+

  • Hoseya 6:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Kodi ndikuchite chiyani iwe Efuraimu? Nanga iwe Yuda, ndikuchite chiyani?+ Anthu inu, kukoma mtima kwanu kosatha ndi kofanana ndi mitambo ya m’mawa, ndiponso ngati mame amene sachedwa kuuma.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena