Ekisodo 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako Farao anatumiza atumiki ake kukaitana Mose ndi Aroni ndi kuwauza kuti: “Tsopano ndachimwa.+ Yehova ndi wolungama,+ koma ine ndi anthu anga ndife olakwa. Salimo 89:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chilungamo ndi chiweruzo ndizo maziko a mpando wanu wachifumu.+Kukoma mtima kosatha ndi choonadi zili pamaso panu.+ Yeremiya 50:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu anga adyedwa ndi aliyense wowapeza,+ ndipo adani awo anena kuti,+ ‘Sitipalamula mlandu uliwonse, chifukwa iwo achimwira Yehova,+ malo okhalamo chilungamo.+ Achimwira Yehova chiyembekezo cha makolo awo.’”+
27 Kenako Farao anatumiza atumiki ake kukaitana Mose ndi Aroni ndi kuwauza kuti: “Tsopano ndachimwa.+ Yehova ndi wolungama,+ koma ine ndi anthu anga ndife olakwa.
14 Chilungamo ndi chiweruzo ndizo maziko a mpando wanu wachifumu.+Kukoma mtima kosatha ndi choonadi zili pamaso panu.+
7 Anthu anga adyedwa ndi aliyense wowapeza,+ ndipo adani awo anena kuti,+ ‘Sitipalamula mlandu uliwonse, chifukwa iwo achimwira Yehova,+ malo okhalamo chilungamo.+ Achimwira Yehova chiyembekezo cha makolo awo.’”+