Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Hoseya 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pamenepo iye adzathamangira amuna omukonda kwambiriwo, koma sadzawapeza.+ Adzawafunafuna koma sadzawapeza. Ndiyeno adzanena kuti, ‘Ndikufuna kubwerera kwa mwamuna wanga+ woyamba,+ pakuti zinthu zinali kundiyendera bwino nthawi imeneyo kusiyana ndi mmene zilili tsopano.’+

  • Hoseya 8:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ngakhale kuti akulipira akazi ochokera m’mitundu ina,+ ine ndidzasonkhanitsa anthu pamodzi. Kwa kanthawi, iwo adzamva ululu woopsa+ chifukwa cha katundu wolemetsa amene mafumu ndi akalonga asenzetsa anthu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena