Yoswa 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pa ulendo wa 7 wozungulira mzindawo, ansembe aja analiza malipenga awo, ndipo Yoswa anauza asilikaliwo kuti: “Fuulani!+ Pakuti Yehova wakupatsani mzindawu.+ Oweruza 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ine ndikaliza lipenga la nyanga ya nkhosa pamodzi ndi anthu onse a m’gulu langa, nanunso mulize malipenga anu kuzungulira msasa wonse,+ ndipo munene kuti, ‘Nkhondo ya Yehova+ ndi ya Gidiyoni!’”
16 Pa ulendo wa 7 wozungulira mzindawo, ansembe aja analiza malipenga awo, ndipo Yoswa anauza asilikaliwo kuti: “Fuulani!+ Pakuti Yehova wakupatsani mzindawu.+
18 Ine ndikaliza lipenga la nyanga ya nkhosa pamodzi ndi anthu onse a m’gulu langa, nanunso mulize malipenga anu kuzungulira msasa wonse,+ ndipo munene kuti, ‘Nkhondo ya Yehova+ ndi ya Gidiyoni!’”